Katakwe KABAZA Wolemba: Lawrence Kadzitche “Bwanawe, masiku amenewa takhala tikusemphana ngati tidatemera msemphano,” Likisho adatero atafika pakhomo pa Katakwe. “Aise, pajatu ndidayamba bizimezi ya kabaza,” Katakwe...
Author - Lawrence Kadzitche
Katakwe KULALIKIRA M’CHINGEREZI Wolemba: Lawrence Kadzitche Monga mkhalakale mu chikhrisitu, a Topitopi amadziwa kuti zimatheka munthu kusintha khalidwe. Iwo sadali mkhirisitu chabe komanso mkulu wampingo ndipo mu...
Katakwe Akwenyetsa bwana Wolemba: Lawrence Kadzitche Sichachilendo. Madilayivala ambiri amakonda kunamizira kuti ndi mabwana. Akakhala kuti amayendetsa General Manager, nayenso amavala udindowu. Izitu zimakonda kuchitika makamaka...
Katakwe GALIMOTO Wolemba: Lawrence Kadzitche Magalimoto alipo a mitundu iwiri. Ena oti bola kukafika ndi ena oti amalankhula. Katakwe adafika pagalimoto yolankhula, galimoto yapamwamba. Idali yamtundu wofiyira ndipo idali...
Katakwe PALIBE CHINSINSI Wolemba: Lawrence Kadzitche Pali amuna ena amangoti yagwa m’mbale n’ndiwo. Amuna amenewa sasankha pankhani ya azimayi. Amangoti bola wavala siketi. Katakwe adali m’gulu limeneli. Iye...
Katakwe ZINA ZIKATI ZICHITIKE Wolemba: Lawrence Kadzitche Pali mavuto ena omwe munthu umagwamo osati chifukwa choti walakwitsa koma chifukwa chakuti zikuoneka ngati walakwitsa. Zimakhala zoti ngakhale utafotokoza bwanji, palibe...
Katakwe KOLAPA Wolemba: Lawrence Kadzitche Zikafika potero, Chichewa chake amati mlaliki wayaka moto. Pobwereka kunena kwa omwe adakhalapo mkulu wa asing’anga, bambo Eliya, Katakwe adafika pa geji ina-ija yosiya kudya...
Katakwe KU DANSI YA BURNING SPEAR Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe zidamuthina. Sadadziwe choti achite. Kuyambira pomwe adali ku sekondale, iye ankakonda kumvera nyimbo za chamba cha reggae ndipo Burning Spear adali...
Katakwe KASONGO Wolemba: Lawrence Kadzitche Mnyimbo yake yotchedwa Ali Manjamanja, Moses Makawa adayimba kuti ‘Eee awa anali wokoma akubwera kumene, anali wokoma mtima akukwatira pano…koma zonsezi anazisiya poti...
Katakwe ZIKHULUPIRIRO Wolemba: Lawrence Kadzitche Mwana ndi yemwe adadzamutenga Katakwe. “Adadi, anthutu akufuna kuwaotcha anzanu!” mwanayo adafuwula mwankhawa. Katakwe adasiya zomwe ankachita nkuthamangira komwe amaloza...
Katakwe AKUMANA NDI GULANKUMWERE Wolemba: Lawrence Kadzitche Mudali mu bala ija yotchuka ya mu Devil Street. Katakwe adakhala pakona ndi Likisho akumwa mowa, kwinaku akutsuka maso powona asungwana wokopa alendo omwe...
Katakwe A TOPITOPI AMUYALUTSA Wolemba: Lawrence Kadzitche Kwa nonse omwe mumagwira ntchito, mukadzangomva kuti kwabwera wachibale wochokera kumudzi kuntchitoko, dzasiyeni zomwe mukuchita ndikukakumana naye nthawi yomweyo. Kaya...
Katakwe Agwa Mmbuna Wolemba: Lawrence Kadzitche Amati fisi akagwa m’buna salankhula. Amaterotu chifukwa fisi akamapita kokaba mbuzi, amadziwa kuti nthawi ina iliyonse akhoza kukumana ndi zokhoma monga kulasidwa kapena kuphedwa...
Katakwe AMUYERETSA MMASO Wolemba: Lawrence Kadzitche “Make mwana, tsegula,” adatero Katakwe ali dzandidzandi ngati nguli yoti nthawi ina iliyonse isiya kuzweta. “Wafika vwivwivwi mwana wahule!” Mkazi wa Katakwe...
Katakwe LERO NDIKUKAPHA SING’ANGA Wolemba: Lawrence Kadzitche “Ziti? Dolo ngati ine sindingalolere kuyaluka m’tauni muno chifukwa cha iwe,” adakalipa Katakwe. “Na ngati suvomera kuti tipite kwa sing’anga udziwe kuti...
Katakwe ZIYANG’ANA KUNGOLO Wolemba: Lawrence Kadzitche Pa Chichewa, zinthu zikathina, pali mawu ambiri omwe amanenedwa. Ena amati zafika pa mwana wakana phala. Chichewa china amati zafika pa mai wafinyira bere pansi mwana...
Katakwe Receipt Wolemba: Lawrence Kadzitche Zimachitika ndithu mmabanja ambiri. Mwamuna amatha kukhala ndi chibwenzi mkazi wake osanunkhiza olo pang’ono. Katakwe adali uja woti pachingerezi amatchedwa model husband...
Katakwe ABUSA CHEPETSANI KUDABADIKA Wolemba: Lawrence Kadzitche Pali nkhani zina zomwe munthu amakana ngakhale atagwidwa kali kutsaya. Monga umfiti, munthu ngakhale atagwidwa akutamba palibe yemwe amavomera kuti ndi...
Katakwe NYUMBA YA LENDI Wolemba: Lawrence Kadzitche Tidali tinyumba tingapo tamakomo khumi. Kutiona munthu adakaganiza kuti tigwa nthawi ina iliyonse. Tidali tinyumba towonetsa kuti sitimasamalidwa. Bafa ndi chimbudzi chidali...
Katakwe ATAMBWALI SAMETANA Wolemba: Lawrence Kadzitche Ngakhale sadaonetsere, malume ndi zakhali a Katakwewo adachoka pakhomopo mokhumudwa. “Apa ndiye tathana nawo basi,” Katakwe adanyadira. “Sukunama,” mkazi wake...