Katakwe MAI BUSA, MUKHALATU PAMITALA Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adatulukira pakhomo pa mbusayo limodzi ndi mchemwali wake. Mmanja mudali pwitika wonola bwino. “Ali kuti mwamuna wako yemwe amadzitcha kuti...
Category - Katakwe Stories
Katakwe Msolo wa mbala Wolemba: Lawrence Kadzitche Kalekale padali munthu wina yemwe adakacheza kwa mzake. Ali kwa mzakeyo, adakhumbira chigwinjiri. Polephera kupirira, adatola chigwinjiricho nkuchiponya mthumba...
Katakwe Avala Bulauzi Wolemba: Lawrence Kadzitche Makamaka m’mizinda ya Lilongwe ndi Blantyre, pali asungwana ena omwe amati kukada, amasamba n’kutchena n’kukaima m’mbali mwa msewu. Iwowa nthawi zambiri amavala mosasiyana...
Katakwe Nyimbo m’tchalitchi Wolemba: Lawrence Kadzitche Chimavuta akhrisitu ambiri chimakhala chiphamaso. Pofuna kuoneka auzimu kwambiri, amabisa zinthu zambiri zomwe amakonda. Chitsanzo chabwino ndi nyimbo...
Katakwe PAULENDO Lawrence Kadzitche Padali padepoti yabasi ya Wenela. Poyamba, Katakwe adaganiza kuti woyendetsa minibasiyo adangovala ndomayo ngati mwa manyado chabe. Chidali chipewa choluka cha mtundu wofiyira, golide ndi...
Katakwe Akana kulalikira pamaliro Wolemba: Lawrence Kadzitche Nthawi yomwe Katakwe ankaponya khasu lake pa phunzi ndi momwe anthuwo amatulukira. “Abusa kodi mukutalikira?” Mdzibwa adafunsa modabwa akuyang’ana...
Katakwe Kofunsira Mbeta Wolemba: Lawrence Kadzitche Kofunsira mbeta kumakhala kofunika kusamala. Sikusiyana ndi kofunsira chibwenzi. Munthu umayenera kubisa khalidwe lako lenileni mpaka zonse zitatheka. Pokhala...
Katakwe CHOTULUKA M’DZIRA CHIMUGWIRITSA Wolemba: Lawrence Kadzitche Nthawi zina anthufe tikamachita zinthu tiziganiza kuti kodi tsogolo lake lidzakhala lotani. N’chifukwa chake amvula zakale amati kupha n’kupha...
Katakwe MOTO WAMACHIRITSO Wolemba: Lawrence Kadzitche Ngati pali utumiki womwe umadyetsa bwino ndi utumiki wamachiritso. Munthu akapemphereredwa n’kuchira nthawi zambiri amakathokoza mbusa womupemphererayo ndi mphatso...
Katakwe KODI TIZIKHALA CHONCHO? Wolemba: Lawrence Kadzitche M’banja lawolo mudali ana asanu. Onse adali pantchito zabwino. Pokhala wachisamba, Katakwe ndi amene adalandira uthengawo. Adatumiza ndi a...
Katakwe TSIKU LA FOTE Wolemba: Lawrence Kadzitche Kaya zidachokera pati koma pa chichewa pali mawu omwe amati tsiku lafote limakwana. Mawuwa amatanthauza kuti munthu ukamachita zachinyengo pakhalekhale tsiku lina...
Katakwe AMAYI AMASIYE Wolemba: Lawrence Kadzitche Nkhani yake idali motere. Udali umodzi mwa mipingo yomweyi yopanda adilesi. Katakwe ndi amene adayambitsa mpingowo ndipo ndiyemwenso adali mbusa wamkulu wa mpingowo. Father and...
Katakwe SONIA ADADZIWA BWANJI? Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adangoti ndapata. Sonia adali msungwana wokongola komanso wakhalidwe losakaikitsa. Nkhani yakhalidwe imachokera poti mtsikanayo adali mtsogoleri wakwaya...
Katakwe NTCHITO ZACHIFUNDO Wolemba: Lawrence Kadzitche A Topitopi adatulutsa kabotolo kaphanthi kuchokera m’thumba la jekete lawo. Adayang’ana pomwe adalekeza bibidayo kenaka n’kuthira kukhosi. Adaipitsa kukamwa...
Katakwe MATENDA A ABUSA Wolemba: Lawrence Kadzitche Akulu ampingowo adasonkhana kuti agwirizane chochita malinga ndi matenda a mbusa wamkulu wampingowo. “Akulu ampingo, monga tonse tikudziwa, abusa athu adwala...
Katakwe KWA ANKHOSWE Wolemba: Lawrence Kadzitche Udali mmawa, dzuwa litangotuluka kumene. Mkazi wa Katakwe adafika limodzi ndi Katakwe kunyumba kwa ankhosweko. Mwana wamkazi adali wokwiya ngati nkhuku yofuna kulandidwa...
Katakwe Vuto lili pati? Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adatulukira pakhomopo ali wefuwefu. Adangofikira kuvula ovololo yake n’kudziponya pampando. “Ndimayendatu mothamanga kuti ndifike nthawi yabwino kuopa mbava,” iye...
Katakwe Panyuwele Wolemba: Lawrence Kadzitche “Mmoyo wanga, Katakwe adatero. Mmoyo wanga, sindidalowepo chaka chatsopano monjoya chomwechi!” Belita adamusisita Katakwe pachifuwa. Nawenso nthabwala! Tsono ukuti...
Katakwe ZOCHITIKA PA KHIRISIMASI Wolemba: Lawrence Kadzitche Pachingerezi amati Christmas Eve. Pachichewa timangoti pa 24 December, tsiku loti mawa ndi khrisimasi. Likisho adatulukira pakhomo pa Katakwe cha ku...
Katakwe Awona malodza Wolemba: Lawrence Kadzitche Mukadzawona malonda akuyalidwa tsiku lilonse ndiye kuti amagulidwa. Katundu wosayenda malonda amachotsedwa pamsika. Motero, mukamayenda usiku n’kuwona...