Katakwe Awona malodza Wolemba: Lawrence Kadzitche Mukadzawona malonda akuyalidwa tsiku lilonse ndiye kuti amagulidwa. Katundu wosayenda malonda amachotsedwa pamsika. Motero, mukamayenda usiku n’kuwona...
Category - Katakwe Stories
Katakwe Mchenga Woyera Wolemba: Lawrence Kadzitche Sabata yonseyo, Katakwe adakhala akutafuna gondolosi, kubwira chiswa ndi kumwa mthibulo womwe adaoda kwa mzimayi uja amagulitsa muti woterewu pafupi ndi banki ija ya ku...
Katakwe KULIMBITSA THUPI Wolemba: Lawrence Kadzitche Amai ena sasiyana ndi mwana. Amati akafuna kanthu, mwamuna wawo nkuwakanira, amakunyuka ngati muja amachitira mwana wotumbwa. Mtundu wa amai akhalidwe lotere ndi aja...
Katakwe CHITHANDIZO CHOLAKWIKA Wolemba: Lawrence Kadzitche Mumzinda wa Blantyre adali mlaliki wamphamvu ndipo adali ndi utumiki wakewake. Tsikulo adali atakwapatira baibulo paulendo wokalalikira ku Makhetha. “Thandizeni...
Katakwe Uthenga pa foni By Lawrence Kadzitche Udali msonkhano wa atsogoleri ampingowo wokambirana zochitika za nyengo ya pasaka. Abusa adali pomwepo ndipo Katakwe, ngati mtsogoleri wa Church Council, ndi amene...
Katakwe AMAI Wolemba: Lawrence Kadzitche Chadzulo lake Katakwe adafika kunyumba kwake mochedwa komanso ataubwira kwambiri. Chidamudzutsa lidali phokoso kuchokera mnyumba yoyandikira. Kenaka adadzamva kugogoda pachitseko...
KATAKWE MKAZI AMUMASULA Wolembe: Lawrence Kadzitche Kaya chidali chipongwe kapena kusalifuna banja, Katakwe adawonjeza. Chichokere chake masiku atatu apitawo, uku kudali kufika kwake. Iye adafika ali dzandidzandi, mowa uli...
Katakwe Minibasi Wolemba: Lawrence Kadzitche A Topitopi adafika mtauni ya Lilongwe kudzaona mphwawo Katakwe yemwe amakhala kwa Chinsapo. Adatsikira musiteji yamabasi akulu nkubuthira bokakwera maminibasi. Akuyandikira...
KUNJA NKWA CORONA Wolemba: Lawrence Kadzitche Lidali dera lachilendo koma Katakwe ndi mkazi wake adapitako kukaona mzawo yemwe adasamukira mbali imeneyo. Adazindikira kuti kumeneko kudalibe magalimoto a matola ndipo njira yokhayo...
Katakwe Kutengeka Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adali paulendo wokagula zinthu mtauni ya Blantyre. Adaimitsa galimoto yake ndipo atangotsika mgalimotoyo adangomva mau akuti, “Katakwe!” Potembenuka, adapeza kuti...
Kwa omwe simudziwa, ngati munthu ukupita ku Lilongwe kuchoka ku Blantyre, pali malo ena pafupi ndi Kameza Roundabout pomwe anthu amakwerera matola opita ku Lilongwe. Katakwe adamutenga mnyamatayo pamenepo. Adali mnyamata wazaka...
Akafika kumabala a ku Chingwirizano, mahule amadziwa kuti tsikulo kuli kusamba mowa komanso ndalama yapadera siyilephera kupezeka. Motero, iwo adamupatsa dzina lakuti Walodi Banki. Dzinalitu lidachokera ku bungwe lija la...
Dzuwa lomwe lidaswa mtengo tsikulo lidali lija lothawitsa buluzi pakhonde kukabisala pamthunzi. Kumwamba kudalibe ndi mtambo womwe ndipo mlengalenga malawi ankavinavina ngati kwapsa moto wolusa. Ngakhale Katakwe ndi mkazi...