Katakwe ZIYANG’ANA KUNGOLO Wolemba: Lawrence Kadzitche Pa Chichewa, zinthu zikathina, pali mawu ambiri omwe amanenedwa. Ena amati zafika pa mwana wakana phala. Chichewa china amati zafika pa mai wafinyira bere pansi mwana...
Stories
Katakwe Receipt Wolemba: Lawrence Kadzitche Zimachitika ndithu mmabanja ambiri. Mwamuna amatha kukhala ndi chibwenzi mkazi wake osanunkhiza olo pang’ono. Katakwe adali uja woti pachingerezi amatchedwa model husband...
Katakwe ABUSA CHEPETSANI KUDABADIKA Wolemba: Lawrence Kadzitche Pali nkhani zina zomwe munthu amakana ngakhale atagwidwa kali kutsaya. Monga umfiti, munthu ngakhale atagwidwa akutamba palibe yemwe amavomera kuti ndi...
Katakwe NYUMBA YA LENDI Wolemba: Lawrence Kadzitche Tidali tinyumba tingapo tamakomo khumi. Kutiona munthu adakaganiza kuti tigwa nthawi ina iliyonse. Tidali tinyumba towonetsa kuti sitimasamalidwa. Bafa ndi chimbudzi chidali...
Katakwe ATAMBWALI SAMETANA Wolemba: Lawrence Kadzitche Ngakhale sadaonetsere, malume ndi zakhali a Katakwewo adachoka pakhomopo mokhumudwa. “Apa ndiye tathana nawo basi,” Katakwe adanyadira. “Sukunama,” mkazi wake...
Katakwe ZINA ZIKACHITIKA Wolemba: Lawrence Kadzitche Anthu ambiri amagwa mmavuto osati chifukwa choti alakwitsa koma chifukwa choti zina zake zachitika zomwe ngakhale atafotokoza bwanji, palibe yemwe...
Katakwe Kokaonekera Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo Katakwe ndi malume ake adatchena ndithu. Lidali tsiku lomwe Maria adalengeza kuti abwera ndi bwenzi lake kudzaonekerera. Thalauza lake latchekitcheki adali atalisita mpaka...
Katakwe Amai, mumaziyamba dala Wolemba: Lawrence Kadzitche Sichikhala chachilendo kuona mwamuna akugulira mkazi wachibwenzi mphatso zosiyanasiyana pomwe kunyumba amangofika chimanjamanja. Amai ambiri samvetsa...
Katakwe DP Wolemba: Lawrence Kadzitche Foni idagwedera. Katakwe adaona kuti idali message ya pa WhatsApp. Idali nambala yachilendo koma ubwino wa WhatsApp, pamakhala chithunzi chija pachingerezi amati Display...
Katakwe Ngombe Yaponda Thope Yamwa Wolemba: Lawrence Kadzitche Mavalidwe a chitenje a amayi amaonetsa mmene zinthu zilili panthawiyo. Akamangira mchiuno mwenimweni ndiye kuti palibe chabwino kapena choipa. Akamangira mmunsi mwa...
Katakwe Khalidwe la Usatana Wolemba: Lawrence Kadzitche Masiku ano kwadza akuti ‘breaking news’. Aliyense akufuna azikhala woyamba kufalitsa nkhani ikachitika. Izi zikumachitika pamasamba amchezo makamaka pa WhatsApp...
Katakwe Nkhani ya Chikondi Wolemba: Lawrence Kadzitche Nthawi yomwe Katakwe ankafika pakhomo pa Likisho, adamuona mzakeyo akulowera kuseri kwa nyumba. Pozungulira khumbilo, Katakwe adadzidzimuka kumuona Likisho...
Katakwe Achimwene, Mwayamba Zisudzo? Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo, pochoka kunyumba, Katakwe adatsanzika kuti akukachita umodzi pabalayo. Mkazi wake, monga mayi womva mwambo, adamulola. Koma m’malo mongoyendera...
Katakwe Mtukula Pakhomo Wolemba: Lawrence Kadzitche Tikhoza kuti chani? Pakhomopo padali phukusi la kasakaniza. Anyamata angapo ankavina ngati muja amachitira ma zombie mu mafilimu. Koma ambiri adali zyoli ngati ali...
Katakwe Chinyengo Chimugwetsa M’mavuto Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adamuona koyamba mayiyo nthawi ya zopereka. Chidamuchititsa chidwi choyamba chidali mayendedwe ake. Sadasiyane n’kuti ali pa catwalk ya fashion...
Katakwe Mavalidwe Mtchalitchi Lawrence Kadzitche Zovala sizionetsa khalidwe la munthu. Nthawi zambiri momwe munthu amavalira amangokhala makonda chabe. Komabe ngakhale izi zili chonchi, zovala zili zonse zimakhala ndi malo...
Katakwe Nthawi Yomweyi Ndalama Yasiya Kuvuta? Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo mkazi wa Katakwe adali m’tauni. Malinga n’kukwera kwa zinthu, ndalama zomwe adatenga sizidakwanire kugula zinthu zomwe ankafuna. Adamuyimbira...
Katakwe AGWA CHAGADA Wolemba: Lawrence Kadzitche Chimasomaso n’choipa. Chimadetsa m’maso. Katakwe adali paulendo wochokera ku Blantyre kupita ku Lunzu. Koma atamuona msungwana yemwe adayima pasiteji ya pa Chileka Round About...
Katakwe MAI BUSA, MUKHALATU PAMITALA Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adatulukira pakhomo pa mbusayo limodzi ndi mchemwali wake. Mmanja mudali pwitika wonola bwino. “Ali kuti mwamuna wako yemwe amadzitcha kuti...
Katakwe Msolo wa mbala Wolemba: Lawrence Kadzitche Kalekale padali munthu wina yemwe adakacheza kwa mzake. Ali kwa mzakeyo, adakhumbira chigwinjiri. Polephera kupirira, adatola chigwinjiricho nkuchiponya mthumba...