Lawrence Kadzitche

Malawian Art Works

  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books
  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books

Stories

  • Katakwe Stories

Katakwe KABAZA

December 20, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
Add Comment

Katakwe KABAZA Wolemba: Lawrence Kadzitche “Bwanawe, masiku amenewa takhala tikusemphana ngati tidatemera msemphano,” Likisho adatero atafika pakhomo pa Katakwe. “Aise, pajatu ndidayamba bizimezi ya kabaza,” Katakwe...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe KULALIKIRA M’CHINGEREZI

December 14, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
10 Comments

Katakwe KULALIKIRA M’CHINGEREZI Wolemba: Lawrence Kadzitche   Monga mkhalakale mu chikhrisitu, a Topitopi amadziwa kuti zimatheka munthu kusintha khalidwe. Iwo sadali mkhirisitu chabe komanso mkulu wampingo ndipo mu...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Akwenyetsa bwana

December 6, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe Akwenyetsa bwana Wolemba: Lawrence Kadzitche Sichachilendo. Madilayivala ambiri amakonda kunamizira kuti ndi mabwana. Akakhala kuti amayendetsa General Manager, nayenso amavala udindowu. Izitu zimakonda kuchitika makamaka...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe GALIMOTO

November 29, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
4 Comments

Katakwe GALIMOTO Wolemba: Lawrence Kadzitche   Magalimoto alipo a mitundu iwiri. Ena oti bola kukafika ndi ena oti amalankhula. Katakwe adafika pagalimoto yolankhula, galimoto yapamwamba. Idali yamtundu wofiyira ndipo idali...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe PALIBE CHINSINSI

November 22, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
4 Comments

Katakwe PALIBE CHINSINSI Wolemba: Lawrence Kadzitche   Pali amuna ena amangoti yagwa m’mbale n’ndiwo. Amuna amenewa sasankha pankhani ya azimayi. Amangoti bola wavala siketi.   Katakwe adali m’gulu limeneli. Iye...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe ZINA ZIKATI ZICHITIKE

November 15, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe ZINA ZIKATI ZICHITIKE Wolemba: Lawrence Kadzitche Pali mavuto ena omwe munthu umagwamo osati chifukwa choti walakwitsa koma chifukwa chakuti zikuoneka ngati walakwitsa. Zimakhala zoti ngakhale utafotokoza bwanji, palibe...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe KOLAPA

November 8, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
2 Comments

Katakwe KOLAPA Wolemba: Lawrence Kadzitche   Zikafika potero, Chichewa chake amati mlaliki wayaka moto. Pobwereka kunena kwa omwe adakhalapo mkulu wa asing’anga, bambo Eliya, Katakwe adafika pa geji ina-ija yosiya kudya...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe KU DANSI YA BURNING SPEAR

November 1, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
3 Comments

Katakwe KU DANSI YA BURNING SPEAR Wolemba: Lawrence Kadzitche   Katakwe zidamuthina. Sadadziwe choti achite. Kuyambira pomwe adali ku sekondale, iye ankakonda kumvera nyimbo za chamba cha reggae ndipo Burning Spear adali...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe KASONGO

October 25, 2024
by Lawrence Kadzitche
4 min read
2 Comments

Katakwe KASONGO Wolemba: Lawrence Kadzitche Mnyimbo yake yotchedwa Ali Manjamanja, Moses Makawa adayimba kuti ‘Eee awa anali wokoma akubwera kumene, anali wokoma mtima akukwatira pano…koma zonsezi anazisiya poti...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe ZIKHULUPIRIRO

October 18, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
6 Comments

Katakwe ZIKHULUPIRIRO Wolemba: Lawrence Kadzitche Mwana ndi yemwe adadzamutenga Katakwe. “Adadi, anthutu akufuna kuwaotcha anzanu!” mwanayo adafuwula mwankhawa. Katakwe adasiya zomwe ankachita nkuthamangira komwe amaloza...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe AKUMANA NDI GULANKUMWERE

October 12, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
3 Comments

Katakwe AKUMANA NDI GULANKUMWERE Wolemba: Lawrence Kadzitche   Mudali mu bala ija yotchuka ya mu Devil Street. Katakwe adakhala pakona ndi Likisho akumwa mowa, kwinaku akutsuka maso powona asungwana wokopa alendo omwe...

Continue reading

  • Uncategorized

Katakwe A TOPITOPI AMUYALUTSA

October 4, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
4 Comments

Katakwe A TOPITOPI AMUYALUTSA Wolemba: Lawrence Kadzitche Kwa nonse omwe mumagwira ntchito, mukadzangomva kuti kwabwera wachibale wochokera kumudzi kuntchitoko, dzasiyeni zomwe mukuchita ndikukakumana naye nthawi yomweyo. Kaya...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Agwa Mmbuna

September 28, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
3 Comments

Katakwe Agwa Mmbuna Wolemba: Lawrence Kadzitche Amati fisi akagwa m’buna salankhula. Amaterotu chifukwa fisi akamapita kokaba mbuzi, amadziwa kuti nthawi ina iliyonse akhoza kukumana ndi zokhoma monga kulasidwa kapena kuphedwa...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe AMUYERETSA MMASO

September 21, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
Add Comment

Katakwe AMUYERETSA MMASO Wolemba: Lawrence Kadzitche “Make mwana, tsegula,” adatero Katakwe ali dzandidzandi ngati nguli yoti nthawi ina iliyonse isiya kuzweta. “Wafika vwivwivwi mwana wahule!” Mkazi wa Katakwe...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe LERO NDIKUKAPHA SING’ANGA

September 14, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
6 Comments

Katakwe LERO NDIKUKAPHA SING’ANGA Wolemba: Lawrence Kadzitche “Ziti? Dolo ngati ine sindingalolere kuyaluka m’tauni muno chifukwa cha iwe,” adakalipa Katakwe. “Na ngati suvomera kuti tipite kwa sing’anga udziwe kuti...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe ZIYANG’ANA KUNGOLO

September 6, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe ZIYANG’ANA KUNGOLO Wolemba: Lawrence Kadzitche Pa Chichewa, zinthu zikathina, pali mawu ambiri omwe amanenedwa. Ena amati zafika pa mwana wakana phala. Chichewa china amati zafika pa mai wafinyira bere pansi mwana...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Receipt

August 30, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe Receipt  Wolemba: Lawrence Kadzitche    Zimachitika ndithu mmabanja ambiri. Mwamuna amatha kukhala ndi chibwenzi mkazi wake osanunkhiza olo pang’ono. Katakwe adali uja woti pachingerezi amatchedwa model husband...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe ABUSA CHEPETSANI KUDABADIKA

August 23, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe ABUSA CHEPETSANI KUDABADIKA Wolemba: Lawrence Kadzitche   Pali nkhani zina zomwe munthu amakana ngakhale atagwidwa kali kutsaya. Monga umfiti, munthu ngakhale atagwidwa akutamba palibe yemwe amavomera kuti ndi...

Continue reading

  • Katakwe Stories

NYUMBA YA LENDI

August 16, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
6 Comments

Katakwe NYUMBA YA LENDI Wolemba: Lawrence Kadzitche Tidali tinyumba tingapo tamakomo khumi. Kutiona munthu adakaganiza kuti tigwa nthawi ina iliyonse. Tidali tinyumba towonetsa kuti sitimasamalidwa. Bafa ndi chimbudzi chidali...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe ATAMBWALI SAMETANA

July 26, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
Add Comment

Katakwe ATAMBWALI SAMETANA Wolemba: Lawrence Kadzitche Ngakhale sadaonetsere, malume ndi zakhali a Katakwewo adachoka pakhomopo mokhumudwa. “Apa ndiye tathana nawo basi,” Katakwe adanyadira. “Sukunama,” mkazi wake...

Continue reading

1 2 3 … 8 Next
Copyright © 2025. Created by DSS. Powered by Digital Silicon Systems.
  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books
  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books