Kwa omwe simudziwa, ngati munthu ukupita ku Lilongwe kuchoka ku Blantyre, pali malo ena pafupi ndi Kameza Roundabout pomwe anthu amakwerera matola opita ku Lilongwe. Katakwe adamutenga mnyamatayo pamenepo. Adali mnyamata wazaka...
Category - Katakwe Stories
Akafika kumabala a ku Chingwirizano, mahule amadziwa kuti tsikulo kuli kusamba mowa komanso ndalama yapadera siyilephera kupezeka. Motero, iwo adamupatsa dzina lakuti Walodi Banki. Dzinalitu lidachokera ku bungwe lija la...
Dzuwa lomwe lidaswa mtengo tsikulo lidali lija lothawitsa buluzi pakhonde kukabisala pamthunzi. Kumwamba kudalibe ndi mtambo womwe ndipo mlengalenga malawi ankavinavina ngati kwapsa moto wolusa. Ngakhale Katakwe ndi mkazi...