Katakwe ZINA ZIKACHITIKA Wolemba: Lawrence Kadzitche Anthu ambiri amagwa mmavuto osati chifukwa choti alakwitsa koma chifukwa choti zina zake zachitika zomwe ngakhale atafotokoza bwanji, palibe yemwe...
Author - Lawrence Kadzitche
Katakwe Kokaonekera Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo Katakwe ndi malume ake adatchena ndithu. Lidali tsiku lomwe Maria adalengeza kuti abwera ndi bwenzi lake kudzaonekerera. Thalauza lake latchekitcheki adali atalisita mpaka...
Katakwe Amai, mumaziyamba dala Wolemba: Lawrence Kadzitche Sichikhala chachilendo kuona mwamuna akugulira mkazi wachibwenzi mphatso zosiyanasiyana pomwe kunyumba amangofika chimanjamanja. Amai ambiri samvetsa...
Katakwe DP Wolemba: Lawrence Kadzitche Foni idagwedera. Katakwe adaona kuti idali message ya pa WhatsApp. Idali nambala yachilendo koma ubwino wa WhatsApp, pamakhala chithunzi chija pachingerezi amati Display...
Katakwe Ngombe Yaponda Thope Yamwa Wolemba: Lawrence Kadzitche Mavalidwe a chitenje a amayi amaonetsa mmene zinthu zilili panthawiyo. Akamangira mchiuno mwenimweni ndiye kuti palibe chabwino kapena choipa. Akamangira mmunsi mwa...
Katakwe Khalidwe la Usatana Wolemba: Lawrence Kadzitche Masiku ano kwadza akuti ‘breaking news’. Aliyense akufuna azikhala woyamba kufalitsa nkhani ikachitika. Izi zikumachitika pamasamba amchezo makamaka pa WhatsApp...
Katakwe Nkhani ya Chikondi Wolemba: Lawrence Kadzitche Nthawi yomwe Katakwe ankafika pakhomo pa Likisho, adamuona mzakeyo akulowera kuseri kwa nyumba. Pozungulira khumbilo, Katakwe adadzidzimuka kumuona Likisho...
Katakwe Achimwene, Mwayamba Zisudzo? Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo, pochoka kunyumba, Katakwe adatsanzika kuti akukachita umodzi pabalayo. Mkazi wake, monga mayi womva mwambo, adamulola. Koma m’malo mongoyendera...
Katakwe Mtukula Pakhomo Wolemba: Lawrence Kadzitche Tikhoza kuti chani? Pakhomopo padali phukusi la kasakaniza. Anyamata angapo ankavina ngati muja amachitira ma zombie mu mafilimu. Koma ambiri adali zyoli ngati ali...
Katakwe Chinyengo Chimugwetsa M’mavuto Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adamuona koyamba mayiyo nthawi ya zopereka. Chidamuchititsa chidwi choyamba chidali mayendedwe ake. Sadasiyane n’kuti ali pa catwalk ya fashion...
Katakwe Mavalidwe Mtchalitchi Lawrence Kadzitche Zovala sizionetsa khalidwe la munthu. Nthawi zambiri momwe munthu amavalira amangokhala makonda chabe. Komabe ngakhale izi zili chonchi, zovala zili zonse zimakhala ndi malo...
Katakwe Nthawi Yomweyi Ndalama Yasiya Kuvuta? Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo mkazi wa Katakwe adali m’tauni. Malinga n’kukwera kwa zinthu, ndalama zomwe adatenga sizidakwanire kugula zinthu zomwe ankafuna. Adamuyimbira...
Katakwe AGWA CHAGADA Wolemba: Lawrence Kadzitche Chimasomaso n’choipa. Chimadetsa m’maso. Katakwe adali paulendo wochokera ku Blantyre kupita ku Lunzu. Koma atamuona msungwana yemwe adayima pasiteji ya pa Chileka Round About...
Katakwe MAI BUSA, MUKHALATU PAMITALA Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adatulukira pakhomo pa mbusayo limodzi ndi mchemwali wake. Mmanja mudali pwitika wonola bwino. “Ali kuti mwamuna wako yemwe amadzitcha kuti...
Katakwe Msolo wa mbala Wolemba: Lawrence Kadzitche Kalekale padali munthu wina yemwe adakacheza kwa mzake. Ali kwa mzakeyo, adakhumbira chigwinjiri. Polephera kupirira, adatola chigwinjiricho nkuchiponya mthumba...
Katakwe Avala Bulauzi Wolemba: Lawrence Kadzitche Makamaka m’mizinda ya Lilongwe ndi Blantyre, pali asungwana ena omwe amati kukada, amasamba n’kutchena n’kukaima m’mbali mwa msewu. Iwowa nthawi zambiri amavala mosasiyana...
Katakwe Nyimbo m’tchalitchi Wolemba: Lawrence Kadzitche Chimavuta akhrisitu ambiri chimakhala chiphamaso. Pofuna kuoneka auzimu kwambiri, amabisa zinthu zambiri zomwe amakonda. Chitsanzo chabwino ndi nyimbo...
Katakwe PAULENDO Lawrence Kadzitche Padali padepoti yabasi ya Wenela. Poyamba, Katakwe adaganiza kuti woyendetsa minibasiyo adangovala ndomayo ngati mwa manyado chabe. Chidali chipewa choluka cha mtundu wofiyira, golide ndi...
Katakwe Akana kulalikira pamaliro Wolemba: Lawrence Kadzitche Nthawi yomwe Katakwe ankaponya khasu lake pa phunzi ndi momwe anthuwo amatulukira. “Abusa kodi mukutalikira?” Mdzibwa adafunsa modabwa akuyang’ana...
Katakwe Kofunsira Mbeta Wolemba: Lawrence Kadzitche Kofunsira mbeta kumakhala kofunika kusamala. Sikusiyana ndi kofunsira chibwenzi. Munthu umayenera kubisa khalidwe lako lenileni mpaka zonse zitatheka. Pokhala...