Lawrence Kadzitche

Malawian Art Works

  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books
  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books

Category - Katakwe Stories

  • Katakwe Stories

Katakwe Kokaonekera

July 12, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
4 Comments

Katakwe Kokaonekera Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo Katakwe ndi malume ake adatchena ndithu. Lidali tsiku lomwe Maria adalengeza kuti abwera ndi bwenzi lake kudzaonekerera. Thalauza lake latchekitcheki adali atalisita mpaka...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Amai, mumaziyamba dala

July 5, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe Amai, mumaziyamba dala Wolemba: Lawrence Kadzitche   Sichikhala chachilendo kuona mwamuna akugulira mkazi wachibwenzi mphatso zosiyanasiyana pomwe kunyumba amangofika chimanjamanja.   Amai ambiri samvetsa...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe DP Wolemba: Lawrence Kadzitche

June 28, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
12 Comments

Katakwe DP Wolemba: Lawrence Kadzitche   Foni idagwedera. Katakwe adaona kuti idali message ya pa WhatsApp.   Idali nambala yachilendo koma ubwino wa WhatsApp, pamakhala chithunzi chija pachingerezi amati Display...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Ngombe Yaponda Thope Yamwa

June 21, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
7 Comments

Katakwe Ngombe Yaponda Thope Yamwa Wolemba: Lawrence Kadzitche Mavalidwe a chitenje a amayi amaonetsa mmene zinthu zilili panthawiyo. Akamangira mchiuno mwenimweni ndiye kuti palibe chabwino kapena choipa. Akamangira mmunsi mwa...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Khalidwe la Usatana

June 14, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
3 Comments

Katakwe Khalidwe la Usatana Wolemba: Lawrence Kadzitche Masiku ano kwadza akuti ‘breaking news’. Aliyense akufuna azikhala woyamba kufalitsa nkhani ikachitika. Izi zikumachitika pamasamba amchezo makamaka pa WhatsApp...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Nkhani ya Chikondi

June 8, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
12 Comments

  Katakwe Nkhani ya Chikondi Wolemba: Lawrence Kadzitche   Nthawi yomwe Katakwe ankafika pakhomo pa Likisho, adamuona mzakeyo akulowera kuseri kwa nyumba. Pozungulira khumbilo, Katakwe adadzidzimuka kumuona Likisho...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Achimwene, Mwayamba Zisudzo?

June 1, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
8 Comments

Katakwe Achimwene, Mwayamba Zisudzo? Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo, pochoka kunyumba, Katakwe adatsanzika kuti akukachita umodzi pabalayo. Mkazi wake, monga mayi womva mwambo, adamulola. Koma m’malo mongoyendera...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Mtukula Pakhomo

May 24, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
Add Comment

  Katakwe Mtukula Pakhomo Wolemba: Lawrence Kadzitche   Tikhoza kuti chani? Pakhomopo padali phukusi la kasakaniza. Anyamata angapo ankavina ngati muja amachitira ma zombie mu mafilimu. Koma ambiri adali zyoli ngati ali...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Chinyengo Chimugwetsa Mmavuto

May 18, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
Add Comment

  Katakwe Chinyengo Chimugwetsa M’mavuto Wolemba: Lawrence Kadzitche Katakwe adamuona koyamba mayiyo nthawi ya zopereka. Chidamuchititsa chidwi choyamba chidali mayendedwe ake. Sadasiyane n’kuti ali pa catwalk ya fashion...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Mavalidwe Mtchalitchi

May 11, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
8 Comments

Katakwe Mavalidwe Mtchalitchi Lawrence Kadzitche   Zovala sizionetsa khalidwe la munthu. Nthawi zambiri momwe munthu amavalira amangokhala makonda chabe. Komabe ngakhale izi zili chonchi, zovala zili zonse zimakhala ndi malo...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Nthawi Yomweyi Ndalama Yasiya Kuvuta?

May 4, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
2 Comments

Katakwe Nthawi Yomweyi Ndalama Yasiya Kuvuta? Wolemba: Lawrence Kadzitche Tsikulo mkazi wa Katakwe adali m’tauni. Malinga n’kukwera kwa zinthu, ndalama zomwe adatenga sizidakwanire kugula zinthu zomwe ankafuna. Adamuyimbira...

Continue reading

  • Katakwe Stories

MAI BUSA, MUKHALATU PAMITALA

April 19, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
4 Comments

Katakwe MAI BUSA, MUKHALATU PAMITALA Wolemba: Lawrence Kadzitche   Katakwe adatulukira pakhomo pa mbusayo limodzi ndi mchemwali wake. Mmanja mudali pwitika wonola bwino.   “Ali kuti mwamuna wako yemwe amadzitcha kuti...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Msolo wa mbala

April 13, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
6 Comments

Katakwe Msolo wa mbala Wolemba: Lawrence Kadzitche   Kalekale padali munthu wina yemwe adakacheza kwa mzake. Ali kwa mzakeyo, adakhumbira chigwinjiri. Polephera kupirira, adatola chigwinjiricho nkuchiponya mthumba...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe- Avala Bulauzi

April 5, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
Add Comment

Katakwe Avala Bulauzi Wolemba: Lawrence Kadzitche Makamaka m’mizinda ya Lilongwe ndi Blantyre, pali asungwana ena omwe amati kukada, amasamba n’kutchena n’kukaima m’mbali mwa msewu. Iwowa nthawi zambiri amavala mosasiyana...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Nyimbo m’tchalitchi

March 30, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
2 Comments

Katakwe Nyimbo m’tchalitchi Wolemba: Lawrence Kadzitche   Chimavuta akhrisitu ambiri chimakhala chiphamaso. Pofuna kuoneka auzimu kwambiri, amabisa zinthu zambiri zomwe amakonda.   Chitsanzo chabwino ndi nyimbo...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe- Paulendo

March 22, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
9 Comments

Katakwe PAULENDO Lawrence Kadzitche Padali padepoti yabasi ya Wenela. Poyamba, Katakwe adaganiza kuti woyendetsa minibasiyo adangovala ndomayo ngati mwa manyado chabe. Chidali chipewa choluka cha mtundu wofiyira, golide ndi...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe Akana kulalikira pamaliro

March 16, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
4 Comments

Katakwe Akana kulalikira pamaliro Wolemba: Lawrence Kadzitche   Nthawi yomwe Katakwe ankaponya khasu lake pa phunzi ndi momwe anthuwo amatulukira.   “Abusa kodi mukutalikira?” Mdzibwa adafunsa modabwa akuyang’ana...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe- Kofunsira Mbeta

March 8, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
Add Comment

Katakwe Kofunsira Mbeta Wolemba: Lawrence Kadzitche   Kofunsira mbeta kumakhala kofunika kusamala. Sikusiyana ndi kofunsira chibwenzi. Munthu umayenera kubisa khalidwe lako lenileni mpaka zonse zitatheka.   Pokhala...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe-M’DZIRA CHIMUGWIRITSA

March 1, 2024
by Lawrence Kadzitche
2 min read
5 Comments

Katakwe CHOTULUKA M’DZIRA CHIMUGWIRITSA Wolemba: Lawrence Kadzitche Nthawi zina anthufe tikamachita zinthu tiziganiza kuti kodi tsogolo lake lidzakhala lotani. N’chifukwa chake amvula zakale amati kupha n’kupha...

Continue reading

  • Katakwe Stories

Katakwe-MOTO WAMACHIRITSO

February 23, 2024
by Lawrence Kadzitche
3 min read
6 Comments

Katakwe MOTO WAMACHIRITSO Wolemba: Lawrence Kadzitche Ngati pali utumiki womwe umadyetsa bwino ndi utumiki wamachiritso. Munthu akapemphereredwa n’kuchira nthawi zambiri amakathokoza mbusa womupemphererayo ndi mphatso...

Continue reading

Previous 1 2 3 4 Next
Copyright © 2025. Created by DSS. Powered by Digital Silicon Systems.
  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books
  • Home
    • About
    • Stories
    • News
    • Media
  • English Short Stories
  • Katakwe Stories
  • Books